Matours International Bus Service Agent

Matours International Bus Service Agent International travel and transport company

27/05/2026

Warning! CHENJEZO

Bus fares from Johannesburg to Malawi remain at:
R1500 BT/LL
R1600 MH
R1700 MZ

Mitengo siinasinthe ayi monga zikunenedwela mmagulupu osiyanasiyana Samalani !!

14/05/2026
08/05/2026

*Masiku Onyamukila ku Johannesburg sanasinthe ayi*

JHB - Blantyre -Thursday and Sunday
JHB -Lilongwe -Thursday and Sunday
JHB-Mangochi-Wednesday and Saturday
JHB-Mzuzu-Wednesday and Saturday

21/04/2026

Tsopano mukhoza kudula ticket, kukwela kapena kutsikila bus pa Kasungu, Office ili pa filling station ya Energem pa Boma Mtengo wa ticket Ndi K270,000, press Whatsapp kuti mumve zambiri

Musaopele kutali Mitengo inatsikaJHB - BT (R1500)JHB - LL (R1500)JHB - MH (R1600)JHB - Mzimba/Mzuzu - R1700 Press the Wh...
17/04/2026

Musaopele kutali Mitengo inatsika
JHB - BT (R1500)
JHB - LL (R1500)
JHB - MH (R1600)
JHB - Mzimba/Mzuzu - R1700

Press the Whatsapp button to book and reserve your seat now

16/04/2026

Tsopano nthawi yonyamukila bus kuno ku Matours ndi 7am ndipo check in time ndi 6am pamaulendo onse ochokera ku Johannesburg
Press Whatsapp to book and reserve your seat

TRUCK UPDATE Tsopano Truck yafika Pamwanza border ndipo ipangidwa clear mmawaZikomo!
30/03/2026

TRUCK UPDATE
Tsopano Truck yafika Pamwanza border ndipo ipangidwa clear mmawa
Zikomo!

Truck updateKwa onse amene anakweza katundu mu truck Mukudziwitsidwa kuti chombochi tsopano chaoloka Nyamapanda kulowa m...
29/03/2026

Truck update
Kwa onse amene anakweza katundu mu truck
Mukudziwitsidwa kuti chombochi tsopano chaoloka Nyamapanda kulowa mmozambique Side update ina ibwera mmawa masana, zikomo!!

26/03/2026

Mukakumana ndi munthu aliyense nkumakuuzani kuti akutengani opanda passport pa bus ya Matours tichitileni whatsapp mwachangu kapena kamunenezeni ku Police yomwe mulinayo pafupi, Matours Siimatenga munthu opanda passport

Address

2 School Street, City And Suburban
Johannesburg

Opening Hours

Monday 07:00 - 17:00
Tuesday 07:00 - 17:00
Wednesday 07:00 - 17:00
Thursday 07:00 - 17:00
Friday 07:00 - 17:00
Saturday 07:00 - 16:00
Sunday 07:00 - 12:00

Telephone

+27717313612

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Matours International Bus Service Agent posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share