Business Logistics Express

Business Logistics Express transport and freight management

Mphini yobwereza kuwala. Kwakoma ndikuno chifukwa kwatchipa. Tiyeni tinyamukeso Saturday tizipita basi
10/12/2025

Mphini yobwereza kuwala. Kwakoma ndikuno chifukwa kwatchipa. Tiyeni tinyamukeso Saturday tizipita basi

Yaboooka yaboooka indeeee yaboooka.Kamtengo pang'ono ulendo kukafika safely. Ndi R1800 ulendo mukafika mukakhalaso ndi c...
08/12/2025

Yaboooka yaboooka indeeee yaboooka.
Kamtengo pang'ono ulendo kukafika safely. Ndi R1800 ulendo mukafika mukakhalaso ndi change chogawa mudzi onse pa Xmas. Kwabeba ndikunooooooooo!!!!

08/12/2025

Tiyeni tinyamuke on Wednesday.

Lilongwe-joburg
Blantyre-joburg
Joburg-Lilongwe
Joburg-Blantyre

Bus yoyenda mosapikisana ndi anthu, yodziwa kuti yanyamula miyoyo ya anthu ofunikira kwambiri ndipo akuyenera kukafika bwino. Ndege zapansi yatchipa ndi December yu.

16/11/2025

Kodi mwamvaaaa?!!!!
Malingana ndi Xmas 🎄 ikubwerayi mitengo yathu ya ndege zapansi tatsitsa kuti anthu musavutike kupita holiday.....dzaduleni ma tickets motchipa Malo asanathe paja azungu amati first come first serve

21/10/2025

KX68RT just passed NYL plaza after zebetelia. Lilongwe to Joburg. Ndege zapansi. Ma customer athu akadye lunch patheba lero

05/08/2025

JHB-LL
LL-JHB
JHB-BT
BT-JHB

Tiyeni tinyamuke mawa. Bus ndiyomweyi sitikusintha

21/07/2025

All the buses are on the roads ena azifika lero ena mawa (Malawi & RSA) konse. Truck 1 yakatundu nayo is on its way to jhb. Ulendo tamfika. Bwerani dzaduleni ma ticket ulendo lachitatu uliposo ndipo katunduyo zibweresani azipita kofunikako. Be safe with Business Logistics Express

28/06/2025

JHB bus KX68RXGP at Dedza boarder now...we are here kuchoka kuthebatu kufika dzuwa lili phwee

03/03/2025

Tibwere kwanuko tidzatenge katunduyo azipita kumudzi? Azanu akutumizatu. No headaches with us. Kutumiza lero katundu 2 days wafika, osati kutenga katundu lero kutha mwezi asanafike mpaka nthochi kupsera mnjira chifukwa chochedwa nononono kuno sitimachedwa.

31/01/2025

Tiyeni tikalandire katundu wathu Sunday li kumalawi basi....ndege zapansi tanyamuka. B.L.E

30/01/2025

Basi tiyeni tizipita komwe tikufuna using Business logistics express. Ma bus okwera ndiomwewa sitikusintha.

Dzakwereni ndege zapansi tizipita basi.
14/01/2025

Dzakwereni ndege zapansi tizipita basi.

Address

149 Pritchard Street
Johannesburg

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Business Logistics Express posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share